-
Levitiko 14:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Pa tsiku la 7 azimeta tsitsi lake lonse lakumutu, ndevu zake zonse ndi nsidze zonse. Akamaliza kumeta tsitsi lake lonse azichapa zovala zake nʼkusamba mʼmadzi ndipo adzakhala woyera.
-
-
Numeri 19:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Munthu woteroyo azidziyeretsa ndi madzi oyeretsera aja pa tsiku lachitatu, ndipo pa tsiku la 7 azikhala woyera. Koma akapanda kudziyeretsa pa tsiku lachitatu, sadzakhala woyera pa tsiku la 7.
-