Salimo 73:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma ine mapazi anga anangotsala pangʼono kusochera,Mapazi anga anangotsala pangʼono kuterereka.+ Aheberi 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chenjerani abale kuti pakati panu, wina asachoke kwa Mulungu wamoyo nʼkukhala ndi mtima woipa wopanda chikhulupiriro.+ 2 Petulo 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho inu okondedwa, popeza mwadziwiratu zimenezi, chenjerani kuti anthu ophwanya malamulowo asakusocheretseni ndi zochita zawo zoipa nʼkuchititsa kuti mugwe chifukwa cholephera kukhala olimba.+
12 Chenjerani abale kuti pakati panu, wina asachoke kwa Mulungu wamoyo nʼkukhala ndi mtima woipa wopanda chikhulupiriro.+
17 Choncho inu okondedwa, popeza mwadziwiratu zimenezi, chenjerani kuti anthu ophwanya malamulowo asakusocheretseni ndi zochita zawo zoipa nʼkuchititsa kuti mugwe chifukwa cholephera kukhala olimba.+