Aheberi 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Nʼchifukwa chake zinthu zimene tinamva tiyenera kuziganizira mozama kuposa nthawi zonse,+ kuti tisatengeke pangʼonopangʼono nʼkusiya chikhulupiriro.+
2 Nʼchifukwa chake zinthu zimene tinamva tiyenera kuziganizira mozama kuposa nthawi zonse,+ kuti tisatengeke pangʼonopangʼono nʼkusiya chikhulupiriro.+