Aheberi 11:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Onsewa anafa ali ndi chikhulupiriro, ngakhale kuti malonjezowo sanakwaniritsidwe pa nthawi yawo.+ Koma anawaona ali patali+ ndipo anawalandira. Analengezanso poyera kuti iwo anali alendo komanso anthu osakhalitsa mʼdzikolo.
13 Onsewa anafa ali ndi chikhulupiriro, ngakhale kuti malonjezowo sanakwaniritsidwe pa nthawi yawo.+ Koma anawaona ali patali+ ndipo anawalandira. Analengezanso poyera kuti iwo anali alendo komanso anthu osakhalitsa mʼdzikolo.