Genesis 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pambuyo pake, Mulungu anauza Nowa kuti: “Ndaganiza zowononga anthu onse, chifukwa apangitsa kuti dziko lapansi lidzaze ndi chiwawa. Choncho ndiwawononga limodzi ndi zonse zimene zili padziko lapansi.+ Genesis 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ine ndidzabweretsa chigumula+ padziko lapansi kuti chiwononge chamoyo chilichonse cha pansi pa thambo, chimene chili ndi mpweya wa moyo* mʼthupi lake. Chilichonse chimene chili padziko lapansi chidzawonongedwa.+
13 Pambuyo pake, Mulungu anauza Nowa kuti: “Ndaganiza zowononga anthu onse, chifukwa apangitsa kuti dziko lapansi lidzaze ndi chiwawa. Choncho ndiwawononga limodzi ndi zonse zimene zili padziko lapansi.+
17 Ine ndidzabweretsa chigumula+ padziko lapansi kuti chiwononge chamoyo chilichonse cha pansi pa thambo, chimene chili ndi mpweya wa moyo* mʼthupi lake. Chilichonse chimene chili padziko lapansi chidzawonongedwa.+