Aheberi 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma tsopano akufunitsitsa malo abwino kwambiri, amene ndi akumwamba. Choncho Mulungu sachita manyazi kutchulidwa kuti Mulungu wawo,+ ndipo wawakonzera mzinda.+
16 Koma tsopano akufunitsitsa malo abwino kwambiri, amene ndi akumwamba. Choncho Mulungu sachita manyazi kutchulidwa kuti Mulungu wawo,+ ndipo wawakonzera mzinda.+