Aheberi 11:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chifukwa ankayembekezera mzinda wokhala ndi maziko enieni, mzinda umene wokonza mapulani ake ndiponso kuumanga ndi Mulungu.+ Aheberi 12:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma mwafika kuphiri la Ziyoni+ ndi mzinda wa Mulungu wamoyo, Yerusalemu wakumwamba,+ kumene kuli angelo ambirimbiri,*
10 Chifukwa ankayembekezera mzinda wokhala ndi maziko enieni, mzinda umene wokonza mapulani ake ndiponso kuumanga ndi Mulungu.+
22 Koma mwafika kuphiri la Ziyoni+ ndi mzinda wa Mulungu wamoyo, Yerusalemu wakumwamba,+ kumene kuli angelo ambirimbiri,*