-
Genesis 22:1, 2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Pambuyo pa zimenezi, Mulungu woona anamuyesa+ Abulahamu ndipo anati: “Abulahamu!” Iye anayankha kuti: “Ine mbuyanga!” 2 Kenako Mulungu anamuuza kuti: “Tenga Isaki+ mwana wako mmodzi yekhayo, mwana wako amene umamukonda kwambiriyo,+ ndipo mupite ku Moriya.+ Kumeneko ukamupereke nsembe yopsereza paphiri limene ndidzakuuza.”
-