-
Genesis 22:9, 10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Kenako iwo anafika pamalo amene Mulungu woona anamuuza Abulahamu. Atafika pamalowo, iye anamanga guwa lansembe nʼkuyala nkhuni zija paguwapo. Atatero, anamanga Isaki mwana wakeyo manja ndi miyendo nʼkumugoneka paguwapo, pamwamba pa nkhuni.+ 10 Ndiyeno Abulahamu anatenga mpeni uja kuti aphe mwana wakeyo.+
-