Aroma 8:18, 19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndikuona kuti mavuto amene tikukumana nawo panopa ndi aangʼono powayerekezera ndi ulemerero umene udzaonekere kudzera mwa ife.+ 19 Chifukwa chilengedwe chikuyembekezera mwachidwi nthawi imene ulemerero wa ana a Mulungu udzaonekere.+ 2 Akorinto 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “‘Ndidzakhala bambo anu+ ndipo inu mudzakhala ana anga aamuna ndi aakazi,’+ watero Yehova* Wamphamvuyonse.”
18 Ndikuona kuti mavuto amene tikukumana nawo panopa ndi aangʼono powayerekezera ndi ulemerero umene udzaonekere kudzera mwa ife.+ 19 Chifukwa chilengedwe chikuyembekezera mwachidwi nthawi imene ulemerero wa ana a Mulungu udzaonekere.+
18 “‘Ndidzakhala bambo anu+ ndipo inu mudzakhala ana anga aamuna ndi aakazi,’+ watero Yehova* Wamphamvuyonse.”