Aroma 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Gawanani ndi oyera mogwirizana ndi zimene akusowa.+ Khalani ochereza.+ 1 Timoteyo 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho woyangʼanira ayenera kukhala wopanda chifukwa chomunenezera, mwamuna wa mkazi mmodzi, wosachita zinthu mopitirira malire, woganiza bwino,+ wochita zinthu mwadongosolo, wochereza alendo+ ndiponso wodziwa kuphunzitsa.+
2 Choncho woyangʼanira ayenera kukhala wopanda chifukwa chomunenezera, mwamuna wa mkazi mmodzi, wosachita zinthu mopitirira malire, woganiza bwino,+ wochita zinthu mwadongosolo, wochereza alendo+ ndiponso wodziwa kuphunzitsa.+