Miyambo 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kodi akasupe ako amwazike panja?Ndipo kodi mitsinje yako ya madzi imwazike mʼmabwalo amumzinda?+ Miyambo 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiye mwana wanga, kodi pali chifukwa chilichonse choti uzisangalalira ndi mkazi wamakhalidwe oipa,*Kapena choti uzikumbatirira chifuwa cha mkazi wachiwerewere?*+ Mateyu 5:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Koma ine ndikukuuzani kuti aliyense woyangʼanitsitsa mkazi+ mpaka kumulakalaka, wachita naye kale chigololo mumtima mwake.+
20 Ndiye mwana wanga, kodi pali chifukwa chilichonse choti uzisangalalira ndi mkazi wamakhalidwe oipa,*Kapena choti uzikumbatirira chifuwa cha mkazi wachiwerewere?*+
28 Koma ine ndikukuuzani kuti aliyense woyangʼanitsitsa mkazi+ mpaka kumulakalaka, wachita naye kale chigololo mumtima mwake.+