1 Akorinto 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Muzitsanzira ine, ngati mmene inenso ndimatsanzirira Khristu.+ 2 Atesalonika 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipotu inuyo mukudziwa zimene mukuyenera kuchita potitsanzira,+ chifukwa sitinachite zinthu zosalongosoka pakati panu,
7 Ndipotu inuyo mukudziwa zimene mukuyenera kuchita potitsanzira,+ chifukwa sitinachite zinthu zosalongosoka pakati panu,