Levitiko 16:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ngʼombe yamphongo ya nsembe yamachimo ndi mbuzi ya nsembe yamachimo, zimene magazi ake analowa nawo mʼmalo oyera pokaphimba machimo, azipita nazo kunja kwa msasa ndipo aziwotcha pamoto zikopa zake, nyama ndi ndowe zake.+
27 Ngʼombe yamphongo ya nsembe yamachimo ndi mbuzi ya nsembe yamachimo, zimene magazi ake analowa nawo mʼmalo oyera pokaphimba machimo, azipita nazo kunja kwa msasa ndipo aziwotcha pamoto zikopa zake, nyama ndi ndowe zake.+