Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 4:11, 12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Koma kunena za chikopa cha ngʼombeyo ndi nyama yake yonse pamodzi ndi mutu wake, ziboda zake, matumbo ake ndi ndowe zake,+ 12 kutanthauza ngʼombe yonseyo, aziitenga nʼkupita nayo kunja kwa msasa. Azipita nayo kumalo oyera kumene amataya phulusa* ndipo aziiwotcha pamoto+ wa nkhuni. Aziwotcha ngʼombeyo kumalo otayako phulusa.

  • Aheberi 13:11, 12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Chifukwa nyama zimene magazi ake, mkulu wa ansembe amalowa nawo mʼmalo oyera ngati nsembe ya machimo, amakaziwotcha kunja kwa msasa.+ 12 Choncho nayenso Yesu anakavutikira kunja kwa geti la mzinda+ kuti ayeretse anthu ndi magazi ake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena