Levitiko 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 ng’ombe yonseyo aziitenga ndi kupita nayo kunja kwa msasa.+ Azipita nayo kumalo oyera kumene amataya phulusa losakanizika ndi mafuta+ ndipo aziitentha pamoto wa nkhuni.+ Azitentha ng’ombeyo kumalo otayako phulusa losakanizika ndi mafuta.
12 ng’ombe yonseyo aziitenga ndi kupita nayo kunja kwa msasa.+ Azipita nayo kumalo oyera kumene amataya phulusa losakanizika ndi mafuta+ ndipo aziitentha pamoto wa nkhuni.+ Azitentha ng’ombeyo kumalo otayako phulusa losakanizika ndi mafuta.