Aroma 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chifukwa ngakhale Khristu sankachita zinthu zodzikondweretsa yekha,+ koma anachita zimene Malemba amanena kuti: “Chipongwe cha anthu amene amakunyozani chandigwera.”+ 2 Akorinto 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho ndimasangalala ndi kufooka, kunyozedwa, kusowa zofunika pa moyo, kuzunzidwa ndiponso zovuta zina chifukwa cha Khristu. Chifukwa pamene ndili wofooka, mʼpamene ndimakhala wamphamvu.+ 1 Petulo 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndinu osangalala*+ ngati anthu akukunyozani chifukwa cha dzina la Khristu chifukwa zimenezi zikusonyeza kuti mzimu woyera wa Mulungu komanso ulemerero wake zili pa inu.
3 Chifukwa ngakhale Khristu sankachita zinthu zodzikondweretsa yekha,+ koma anachita zimene Malemba amanena kuti: “Chipongwe cha anthu amene amakunyozani chandigwera.”+
10 Choncho ndimasangalala ndi kufooka, kunyozedwa, kusowa zofunika pa moyo, kuzunzidwa ndiponso zovuta zina chifukwa cha Khristu. Chifukwa pamene ndili wofooka, mʼpamene ndimakhala wamphamvu.+
14 Ndinu osangalala*+ ngati anthu akukunyozani chifukwa cha dzina la Khristu chifukwa zimenezi zikusonyeza kuti mzimu woyera wa Mulungu komanso ulemerero wake zili pa inu.