Mateyu 12:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Chifukwa aliyense amene amachita zimene Atate wanga wakumwamba amafuna, ameneyo ndi mchimwene wanga, mchemwali wanga ndi mayi anga.”+ Aroma 8:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Amatero chifukwa amene anawadziwa choyamba anawasankhiratu kuti adzakhale ofanana ndi Mwana wake,+ kuti iye akhale woyamba kubadwa+ pakati pa abale ake ambiri.+
50 Chifukwa aliyense amene amachita zimene Atate wanga wakumwamba amafuna, ameneyo ndi mchimwene wanga, mchemwali wanga ndi mayi anga.”+
29 Amatero chifukwa amene anawadziwa choyamba anawasankhiratu kuti adzakhale ofanana ndi Mwana wake,+ kuti iye akhale woyamba kubadwa+ pakati pa abale ake ambiri.+