Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 7:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Chonde, thetsani zinthu zoipa zimene anthu oipa akuchita.

      Koma muchititse kuti wolungama akhale wolimba,+

      Chifukwa inu ndinu Mulungu wolungama+ amene amayeza mitima+ komanso mmene munthu akumvera mumtima.*+

  • Salimo 90:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Mumaika zolakwa zathu patsogolo panu,*+

      Zinsinsi zathu zaululika chifukwa cha kuwala kwa nkhope yanu.+

  • Miyambo 15:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ngati Yehova amaona bwinobwino amene ali mʼManda* ndiponso malo achiwonongeko,*+

      Ndiye kuli bwanji zimene zili mʼmitima ya anthu?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena