Yeremiya 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ine Yehova ndimafufuza mtima,+Ndimafufuza maganizo a mkati mwa mtima wa munthu,*Kuti munthu aliyense ndimuchitire zinthu mogwirizana ndi zochita zake,Komanso mogwirizana ndi zipatso za ntchito zake.+ Aheberi 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Palibe cholengedwa chimene Mulungu sangathe kuchiona.+ Chifukwa kwa iye zinthu zonse zili poonekera ndipo amatha kuziona bwinobwino moti ifeyo tidzayankha kwa Mulunguyo pa zochita zathu.+
10 Ine Yehova ndimafufuza mtima,+Ndimafufuza maganizo a mkati mwa mtima wa munthu,*Kuti munthu aliyense ndimuchitire zinthu mogwirizana ndi zochita zake,Komanso mogwirizana ndi zipatso za ntchito zake.+
13 Palibe cholengedwa chimene Mulungu sangathe kuchiona.+ Chifukwa kwa iye zinthu zonse zili poonekera ndipo amatha kuziona bwinobwino moti ifeyo tidzayankha kwa Mulunguyo pa zochita zathu.+