Machitidwe 17:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Chifukwa wakhazikitsa tsiku limene akufuna kudzaweruza+ mwachilungamo dziko lonse lapansi, kudzera mwa munthu amene iye wamusankha. Ndipo watsimikizira anthu onse zimenezi pomuukitsa.”+ Aroma 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Zimenezi zidzaonekera pa tsiku limene Mulungu, kudzera mwa Khristu Yesu, adzaweruze zinthu zachinsinsi zimene anthu amachita komanso kuganiza.+ Ndipo adzaweruza mogwirizana ndi uthenga wabwino umene ndikulalikira. Aroma 14:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho aliyense wa ife adzayankha yekha kwa Mulungu.+
31 Chifukwa wakhazikitsa tsiku limene akufuna kudzaweruza+ mwachilungamo dziko lonse lapansi, kudzera mwa munthu amene iye wamusankha. Ndipo watsimikizira anthu onse zimenezi pomuukitsa.”+
16 Zimenezi zidzaonekera pa tsiku limene Mulungu, kudzera mwa Khristu Yesu, adzaweruze zinthu zachinsinsi zimene anthu amachita komanso kuganiza.+ Ndipo adzaweruza mogwirizana ndi uthenga wabwino umene ndikulalikira.