Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 39:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Zoonadi, moyo wa munthu aliyense umangodutsa ngati chithunzithunzi.

      Iye amangovutika* popanda phindu.

      Amaunjika chuma, osadziwa kuti amene adzasangalale nacho ndi ndani.+

  • Miyambo 27:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Usadzitame ndi zimene udzachite mawa

      Chifukwa sukudziwa zimene zidzachitike mawa.*+

  • Mlaliki 6:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndi ndani akudziwa zinthu zabwino zimene munthu angachite pa masiku ochepa a moyo wake wachabechabe, umene umakhala ngati mthunzi?+ Chifukwa ndi ndani angauze munthu zimene zidzachitike padziko lapansi pano iyeyo atafa?

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena