Mateyu 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mudzawazindikira chifukwa cha zipatso zawo. Anthu sathyola mphesa paminga kapena nkhuyu pamtengo wa nthula, amatero kodi?+
16 Mudzawazindikira chifukwa cha zipatso zawo. Anthu sathyola mphesa paminga kapena nkhuyu pamtengo wa nthula, amatero kodi?+