-
1 Timoteyo 5:1, 2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Usadzudzule mokalipa mwamuna wachikulire,+ koma uzilankhula naye mokoma mtima ngati bambo ako. Amuna achinyamata uzilankhula nawo ngati achimwene ako 2 ndipo akazi achikulire ngati amayi ako. Akazi achitsikana uzilankhula nawo ngati achemwali ako, ndipo pochita zimenezi usakhale ndi maganizo alionse olakwika.
-