1 Timoteyo 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Usadzudzule mwamuna wachikulire mokalipa,+ koma umudandaulire ngati bambo ako. Amuna achinyamata uwadandaulire ngati abale ako, 1 Timoteyo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:1 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),8/2018, tsa. 11 Nsanja ya Olonda,6/1/1987, tsa. 5
5 Usadzudzule mwamuna wachikulire mokalipa,+ koma umudandaulire ngati bambo ako. Amuna achinyamata uwadandaulire ngati abale ako,