Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 15:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Kuyankha modekha* kumabweza mkwiyo,+

      Koma mawu opweteka amayambitsa mkwiyo.+

  • 2 Timoteyo 2:24, 25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Kapolo wa Ambuye sayenera kukangana ndi anthu. Koma ayenera kukhala wodekha kwa onse,+ woyenerera kuphunzitsa, wougwira mtima ena akamulakwira+ 25 ndiponso wotha kulangiza mofatsa anthu otsutsa+ kuti mwina Mulungu angawalole kulapa* nʼkudziwa choonadi molondola.+

  • Tito 3:1, 2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pitiriza kuwakumbutsa kuti azigonjera ndiponso kumvera maboma ndi olamulira.+ Akhalenso okonzeka kugwira ntchito iliyonse yabwino. 2 Asamanenere zoipa munthu aliyense ndiponso asamakonde kukangana. Koma akhale ololera+ ndipo azikhala ofatsa kwa anthu onse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena