Aefeso 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Valani zida zonse zankhondo+ zochokera kwa Mulungu kuti musagonje polimbana ndi zochita zachinyengo* za Mdyerekezi, Yakobo 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho gonjerani Mulungu,+ koma tsutsani Mdyerekezi+ ndipo adzakuthawani.+
11 Valani zida zonse zankhondo+ zochokera kwa Mulungu kuti musagonje polimbana ndi zochita zachinyengo* za Mdyerekezi,