Yesaya 53:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye ananyozedwa ndipo anthu ankamupewa,+Anali munthu amene kupweteka ankakudziwa bwino* ndipo matenda ankawadziwa. Zinali ngati kuti nkhope yake yabisika kwa ife.* Ananyozedwa ndipo tinkamuona ngati wopanda pake.+ Yohane 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma iwo anafuula kuti: “Muthane naye! Muthane naye! Apachikidwe ameneyo!”* Pilato anawafunsa kuti: “Kodi ndipachike mfumu yanu?” Ansembe aakulu anayankha kuti: “Tilibe mfumu ina koma Kaisara.”
3 Iye ananyozedwa ndipo anthu ankamupewa,+Anali munthu amene kupweteka ankakudziwa bwino* ndipo matenda ankawadziwa. Zinali ngati kuti nkhope yake yabisika kwa ife.* Ananyozedwa ndipo tinkamuona ngati wopanda pake.+
15 Koma iwo anafuula kuti: “Muthane naye! Muthane naye! Apachikidwe ameneyo!”* Pilato anawafunsa kuti: “Kodi ndipachike mfumu yanu?” Ansembe aakulu anayankha kuti: “Tilibe mfumu ina koma Kaisara.”