Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 118:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Mwala umene omanga nyumba anaukana

      Wakhala mwala wapakona* wofunika kwambiri.+

  • Yesaya 42:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Taonani mtumiki wanga+ amene ndikumuthandiza,

      Wosankhidwa wanga+ amene amandisangalatsa,+

      Ine ndaika mzimu wanga mwa iye.+

      Iye adzabweretsa chilungamo kwa anthu a mitundu ina.+

  • Mateyu 21:42
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Ndiyeno Yesu anawauza kuti: “Paja Malemba amanena kuti, ‘Mwala umene omanga nyumba anaukana wakhala mwala wapakona wofunika kwambiri.*+ Umenewu wachokera kwa Yehova* ndipo ndi wodabwitsa mʼmaso mwathu.+ Kodi simunawerenge zimeneziʼ?

  • Machitidwe 4:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Yesu ameneyu ndi ‘mwala umene inu omanga nyumba munauona ngati wopanda pake, umene tsopano wakhala mwala wofunika kwambiri wapakona.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena