1 Yohane 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Munthu amene amanena kuti ali mʼkuwala koma amadana+ ndi mʼbale wake, ndiye kuti adakali mumdima.+ Chivumbulutso 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iwe ukunena kuti: “Ndine wolemera,+ ndapeza chuma chambiri ndipo sindikusowa kanthu,” koma sukudziwa kuti ndiwe wovutika, womvetsa chisoni, wosauka, wakhungu ndiponso wamaliseche.
17 Iwe ukunena kuti: “Ndine wolemera,+ ndapeza chuma chambiri ndipo sindikusowa kanthu,” koma sukudziwa kuti ndiwe wovutika, womvetsa chisoni, wosauka, wakhungu ndiponso wamaliseche.