Aefeso 4:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Chidani chachikulu,+ kupsa mtima, mkwiyo, kulalata, mawu achipongwe+ komanso zinthu zonse zoipa zichotsedwe mwa inu.+ Akolose 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma tsopano muyenera kutaya zonsezo kutali ndi inu. Mutaye mkwiyo, kupsa mtima, kuipa+ komanso mawu achipongwe+ ndipo pakamwa panu pasatuluke nkhani zotukwana.+
31 Chidani chachikulu,+ kupsa mtima, mkwiyo, kulalata, mawu achipongwe+ komanso zinthu zonse zoipa zichotsedwe mwa inu.+
8 Koma tsopano muyenera kutaya zonsezo kutali ndi inu. Mutaye mkwiyo, kupsa mtima, kuipa+ komanso mawu achipongwe+ ndipo pakamwa panu pasatuluke nkhani zotukwana.+