Yuda 17, 18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma inu okondedwa, kumbukirani mawu amene atumwi a Ambuye wathu Yesu Khristu ananeneratu kalero. 18 Paja ankakuuzani kuti: “Mʼmasiku otsiriza kudzakhala onyoza, omwe azidzangochita zinthu zoipa zimene amalakalaka.”+
17 Koma inu okondedwa, kumbukirani mawu amene atumwi a Ambuye wathu Yesu Khristu ananeneratu kalero. 18 Paja ankakuuzani kuti: “Mʼmasiku otsiriza kudzakhala onyoza, omwe azidzangochita zinthu zoipa zimene amalakalaka.”+