Yoweli 2:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Dzuwa lidzasanduka mdima ndipo mwezi udzasanduka magazi,+Tsiku lalikulu ndi lochititsa mantha la Yehova lisanafike.+ Zefaniya 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsiku lalikulu la Yehova lili pafupi.+ Lili pafupi ndipo likubwera mofulumira kwambiri.+ Mkokomo wa tsiku la Yehova ukubwera ndi zowawa.+ Pa tsiku limenelo msilikali adzalira.+
31 Dzuwa lidzasanduka mdima ndipo mwezi udzasanduka magazi,+Tsiku lalikulu ndi lochititsa mantha la Yehova lisanafike.+
14 Tsiku lalikulu la Yehova lili pafupi.+ Lili pafupi ndipo likubwera mofulumira kwambiri.+ Mkokomo wa tsiku la Yehova ukubwera ndi zowawa.+ Pa tsiku limenelo msilikali adzalira.+