1 Yohane 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Palibe amene anaonapo Mulungu.+ Tikapitiriza kukondana, Mulungu apitiriza kukhala nafe ndipo azitisonyeza chikondi chake mokwanira.+
12 Palibe amene anaonapo Mulungu.+ Tikapitiriza kukondana, Mulungu apitiriza kukhala nafe ndipo azitisonyeza chikondi chake mokwanira.+