Aheberi 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho, tiyeni tizifika kumpando wachifumu wa Mulungu ndipo tizipemphera ndi ufulu wa kulankhula+ kuti atichitire chifundo komanso kutisonyeza kukoma mtima kwakukulu pa nthawi yoyenera. 1 Yohane 3:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Okondedwa, ngati mitima yathu sikutitsutsa, tikhoza kulankhula momasuka ndi Mulungu.+
16 Choncho, tiyeni tizifika kumpando wachifumu wa Mulungu ndipo tizipemphera ndi ufulu wa kulankhula+ kuti atichitire chifundo komanso kutisonyeza kukoma mtima kwakukulu pa nthawi yoyenera.