1 Yohane 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ana inu, ino ndi nthawi yakumapeto. Munamva kuti wokana Khristu akubwera,+ ndipo panopa okana Khristu ambiri aonekera.+ Chifukwa cha zimenezi tikudziwa kuti ino ndi nthawi yakumapeto.
18 Ana inu, ino ndi nthawi yakumapeto. Munamva kuti wokana Khristu akubwera,+ ndipo panopa okana Khristu ambiri aonekera.+ Chifukwa cha zimenezi tikudziwa kuti ino ndi nthawi yakumapeto.