Yohane 13:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndikukupatsani lamulo latsopano, kuti muzikondana. Mofanana ndi mmene ine ndakukonderani,+ inunso muzikondana choncho.+ 1 Yohane 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Okondedwa, sindikukulemberani lamulo latsopano. Koma ndikukulemberani lamulo lakale limene mwakhala nalo kuyambira pachiyambi.+ Lamulo lakaleli ndi mawu amene munawamva. 2 Yohane 5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chotero ndikukupemphani mayi, kuti tizikondana. (Sindikukulemberani lamulo latsopano, koma lomwe lija limene takhala nalo kuyambira pachiyambi.)+
34 Ndikukupatsani lamulo latsopano, kuti muzikondana. Mofanana ndi mmene ine ndakukonderani,+ inunso muzikondana choncho.+
7 Okondedwa, sindikukulemberani lamulo latsopano. Koma ndikukulemberani lamulo lakale limene mwakhala nalo kuyambira pachiyambi.+ Lamulo lakaleli ndi mawu amene munawamva.
5 Chotero ndikukupemphani mayi, kuti tizikondana. (Sindikukulemberani lamulo latsopano, koma lomwe lija limene takhala nalo kuyambira pachiyambi.)+