Mateyu 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndinu osangalala pamene anthu akukunyozani,+ kukuzunzani komanso kukunamizirani+ zoipa zilizonse chifukwa cha ine.+ Yohane 15:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ngati dziko likudana nanu, muzikumbukira kuti linayamba kudana ndi ine lisanadane ndi inu.+ 2 Timoteyo 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pajatu onse ofuna kukhala ndi moyo wodzipereka kwa Mulungu mogwirizana ndi Khristu Yesu, nawonso adzazunzidwa.+
11 Ndinu osangalala pamene anthu akukunyozani,+ kukuzunzani komanso kukunamizirani+ zoipa zilizonse chifukwa cha ine.+
12 Pajatu onse ofuna kukhala ndi moyo wodzipereka kwa Mulungu mogwirizana ndi Khristu Yesu, nawonso adzazunzidwa.+