Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Aroma 8:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Mofanana ndi zimenezi, mzimu umatithandiza pa zimene tikulephera kuchita.+ Chifukwa vuto ndi lakuti sitidziwa zimene tikufunika kutchula popemphera, koma mzimu umachonderera mʼmalo mwathu ndi madandaulo amene sitinathe kuwafotokoza.

  • Aefeso 6:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Pamene mukuchita zimenezi, muzipemphera pa chochitika chilichonse mu mzimu,+ pogwiritsa ntchito pemphero+ ndi pembedzero la mtundu uliwonse. Kuti muchite zimenezi khalani maso ndipo nthawi zonse muzipemphera mopembedzera mʼmalo mwa oyera onse.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena