Yohane 14:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ine ndidzapempha Atate ndipo adzakupatsani mthandizi* wina kuti adzakhale nanu mpaka kalekale.+ Yohane 14:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma mthandizi, amene ndi mzimu woyera umene Atate wanga adzatumize mʼdzina langa, adzakuphunzitsani komanso kukukumbutsani zinthu zonse zimene ndinakuuzani.+ Yohane 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kunena zoona, ndikupita kuti inu mupindule. Chifukwa ngati sindipita ndiye kuti mthandizi uja+ sabwera kwa inu. Koma ndikapita ndikamutumiza kwa inu.
26 Koma mthandizi, amene ndi mzimu woyera umene Atate wanga adzatumize mʼdzina langa, adzakuphunzitsani komanso kukukumbutsani zinthu zonse zimene ndinakuuzani.+
7 Kunena zoona, ndikupita kuti inu mupindule. Chifukwa ngati sindipita ndiye kuti mthandizi uja+ sabwera kwa inu. Koma ndikapita ndikamutumiza kwa inu.