Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Luka 24:49
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 49 Ndipo ine ndidzakutumizirani chimene Atate wanga anakulonjezani. Koma inu mukhalebe mumzindawu mpaka mutalandira mphamvu zochokera kumwamba.”+

  • Yohane 15:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Akadzafika mthandizi amene ndidzakutumizireni kuchokera kwa Atate, amene ndi mzimu wa choonadi+ wochokera kwa Atate, ameneyo adzandichitira umboni,+

  • Yohane 16:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Koma mthandiziyo akadzabwera, amene ndi mzimu wa choonadi,+ adzakutsogolerani mʼchoonadi chonse. Chifukwa sadzalankhula zongoganiza payekha, koma adzalankhula zimene wamva ndipo adzalengeza kwa inu zinthu zimene zikubwera.+

  • 1 Yohane 2:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Koma inuyo, Mulungu anakudzozani ndi mzimu wake+ ndipo mzimu umenewo udakali mwa inu, moti simukufunikira wina aliyense woti azikuphunzitsani. Koma kudzozedwako kukukuphunzitsani zinthu zonse+ ndipo ndi koona osati konama. Monga mmene kudzozedwako kwakuphunzitsirani, pitirizani kukhala ogwirizana naye.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena