Luka 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndikukuuzani kuti, aliyense amene akuvomereza pamaso pa anthu kuti ndi wophunzira wanga,+ Mwana wa munthunso adzamuvomereza pamaso pa angelo a Mulungu kuti ndi wophunzira wake.+
8 Ndikukuuzani kuti, aliyense amene akuvomereza pamaso pa anthu kuti ndi wophunzira wanga,+ Mwana wa munthunso adzamuvomereza pamaso pa angelo a Mulungu kuti ndi wophunzira wake.+