Luka 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma zogwera panthaka yabwino, ndi anthu amene pambuyo pomva mawuwo ndi mtima wabwino kwambiri,+ amawagwiritsitsa nʼkubereka zipatso mopirira.+ Luka 21:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ngati inu mudzapirire, mudzapeza moyo.+ 2 Timoteyo 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tikapitiriza kupirira, tidzalamuliranso naye monga mafumu.+ Tikamukana, iyenso adzatikana,+ Aheberi 10:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Mukufunika kukhala opirira+ komanso kuchita chifuniro cha Mulungu kuti mudzalandire zimene Mulunguyo walonjeza. Aheberi 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho ganizirani mozama za munthu amene anapirira malankhulidwe onyoza amenewo a anthu ochimwa,+ amene polankhula zimenezo ankangodzivulaza okha. Ganizirani za munthu ameneyu kuti musatope nʼkutaya mtima.+
15 Koma zogwera panthaka yabwino, ndi anthu amene pambuyo pomva mawuwo ndi mtima wabwino kwambiri,+ amawagwiritsitsa nʼkubereka zipatso mopirira.+
36 Mukufunika kukhala opirira+ komanso kuchita chifuniro cha Mulungu kuti mudzalandire zimene Mulunguyo walonjeza.
3 Choncho ganizirani mozama za munthu amene anapirira malankhulidwe onyoza amenewo a anthu ochimwa,+ amene polankhula zimenezo ankangodzivulaza okha. Ganizirani za munthu ameneyu kuti musatope nʼkutaya mtima.+