-
Chivumbulutso 21:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Mzindawo unali ndi mpanda waukulu komanso wautali ndipo unali ndi mageti 12. Pamagetiwo panali angelo 12 ndipo panalembedwa mayina a mafuko 12 a ana a Isiraeli.
-