2 Akorinto 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndikukuchitirani nsanje, ngati imene Mulungu amakuchitirani, popeza ndine ndinakuchititsani kulonjezedwa ukwati ndi mwamuna mmodzi, Khristu, ndipo ndikufuna kukuperekani ngati namwali woyera kwa iye.+ Yakobo 1:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kulambira* koyera komanso kosadetsedwa kwa Mulungu ndi Atate wathu ndi uku: Kusamalira ana amasiye+ ndi akazi amasiye+ amene akukumana ndi mavuto*+ komanso kupewa kuti dzikoli likuchititseni kukhala ndi banga.+ Yakobo 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Achigololo inu,* kodi simukudziwa kuti kuchita ubwenzi ndi dziko nʼkudziika pa udani ndi Mulungu? Choncho aliyense amene akufuna kukhala bwenzi la dziko akudzipangitsa kuti akhale mdani wa Mulungu.+
2 Ndikukuchitirani nsanje, ngati imene Mulungu amakuchitirani, popeza ndine ndinakuchititsani kulonjezedwa ukwati ndi mwamuna mmodzi, Khristu, ndipo ndikufuna kukuperekani ngati namwali woyera kwa iye.+
27 Kulambira* koyera komanso kosadetsedwa kwa Mulungu ndi Atate wathu ndi uku: Kusamalira ana amasiye+ ndi akazi amasiye+ amene akukumana ndi mavuto*+ komanso kupewa kuti dzikoli likuchititseni kukhala ndi banga.+
4 Achigololo inu,* kodi simukudziwa kuti kuchita ubwenzi ndi dziko nʼkudziika pa udani ndi Mulungu? Choncho aliyense amene akufuna kukhala bwenzi la dziko akudzipangitsa kuti akhale mdani wa Mulungu.+