-
Salimo 75:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
Ndithudi, iye adzakhuthula vinyo yense
Ndipo anthu onse oipa padziko lapansi adzamwa mpaka kugugudiza nsenga zake.”+
-
-
Chivumbulutso 11:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Koma mitundu ya anthu inakwiya ndipo inunso munasonyeza mkwiyo wanu. Ndiye nthawi yoikidwiratu inafika yoti akufa aweruzidwe nʼkupereka mphoto+ kwa akapolo anu aneneri+ komanso kwa oyera ndi amene akuopa dzina lanu, olemekezeka ndi onyozeka omwe. Komanso nthawi yoti muwononge amene akuwononga dziko lapansi.”+
-