Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 19:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Kuopa Yehova+ nʼkoyera, ndipo kudzakhalapo kwamuyaya.

      Zigamulo za Yehova nʼzolondola, ndipo pa mbali iliyonse ndi zolungama.+

  • Salimo 119:137
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 137 Ndinu wolungama, inu Yehova,+

      Ndipo zigamulo zanu ndi zachilungamo.+

  • Chivumbulutso 19:1, 2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Zimenezi zitatha, ndinamva mawu kumwamba amene ankamveka ngati mawu ofuula a khamu lalikulu akuti: “Tamandani Ya!*+ Mulungu wathu amapulumutsa anthu ndipo ali ndi mphamvu zazikulu komanso ulemerero, 2 chifukwa ziweruzo zake ndi zoona ndi zolungama.+ Iye waweruza hule lalikulu limene linaipitsa dziko lapansi ndi chiwerewere* chake, ndipo walibwezera chifukwa cha magazi a akapolo ake, amene hulelo linapha.”*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena