Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 32:43
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 43 Inu anthu a mitundu ina, sangalalani limodzi ndi anthu ake,+

      Chifukwa adzabwezera magazi a atumiki ake,+

      Ndipo adzabwezera chilango kwa adani ake,+

      Komanso adzaphimba machimo a dziko la anthu ake.”*

  • 2 Mafumu 9:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ukaphe anthu a mʼbanja la mbuye wako Ahabu ndipo ine ndidzabwezera magazi a atumiki anga aneneri ndiponso magazi a atumiki onse a Yehova amene Yezebeli anawapha.+

  • Salimo 79:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Musalole kuti anthu a mitundu ina azinena kuti: “Mulungu wawo ali kuti?”+

      Anthu a mitundu ina adziwe ife tikuona

      Kuti mwabwezera magazi a atumiki anu amene anakhetsedwa.+

  • Chivumbulutso 18:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Sangalalani kumwambako chifukwa cha zimene zamuchitikira.+ Inunso oyera,+ atumwi ndi aneneri, sangalalani chifukwa Mulungu wamupatsa chilango chifukwa cha zomwe anakuchitirani.”+

  • Chivumbulutso 18:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Mwa iye munapezeka magazi a aneneri, a oyera,+ ndi a onse amene anaphedwa padziko lapansi.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena