-
Yesaya 44:27, 28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Ndine amene ndikuuza madzi akuya kuti, ‘Iphwa
Ndipo mitsinje yako yonse ndidzaiumitsa.’+
28 Ndine amene ndikunena za Koresi+ kuti, ‘Iye ndi mʼbusa wanga,
Ndipo adzakwaniritsa bwinobwino zonse zimene ndikufuna,’+
Amene ndanena zokhudza Yerusalemu kuti, ‘Adzamangidwanso,’
Ndiponso zokhudza kachisi kuti, ‘Maziko ako adzamangidwa.’”+
-