Chivumbulutso 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakati pa zoikapo nyalezo, panali wina wooneka ngati mwana wa munthu+ atavala chovala chofika kumapazi ndipo anali atamanga lamba wagolide pachifuwa. Chivumbulutso 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Nditamuona, ndinagwera pamapazi ake ngati kuti ndafa. Ndipo anandigwira ndi dzanja lake lamanja nʼkundiuza kuti: “Usachite mantha. Ine ndine Woyamba+ ndi Womaliza,+
13 Pakati pa zoikapo nyalezo, panali wina wooneka ngati mwana wa munthu+ atavala chovala chofika kumapazi ndipo anali atamanga lamba wagolide pachifuwa.
17 Nditamuona, ndinagwera pamapazi ake ngati kuti ndafa. Ndipo anandigwira ndi dzanja lake lamanja nʼkundiuza kuti: “Usachite mantha. Ine ndine Woyamba+ ndi Womaliza,+